Song: Lilime

Artist: kommander Zwangie

Album: Peacock wings

Lyrics

Artist: KOMMANDER ZWANGIE.
SONG: LILIME
GENRE: DANCEHALL.
RECORD LABEL: Royal Peacock musik
PROD: TACKTIC (FRAMECITY)
COMPOSED BY : LIGHTWELL NGWIRA
.
Full lyrics.
.
Intro.
Eyoooh Tactick raise the
volume me affih dweet fih Malawi eti, tchooo.
Linakhala bwanj/(tell me now)
this one kommander zwangie/(u Neva know)
straight outta peacock.(good vibes wer pree)Tchooooo.

.._(bridge)
.
limathokoza/(sometimes)
lomwelo limanyoza/( sometimes)
mbiri liipitsa /( sometimes) Pena kulimbikitsa eey/( sometimes)
kachiwalo kokhala mumlomo/(think about it)
me tell yah say kanadzadza ndi uchimo/ (Lilime lakolo aise)
analipanga bwanj lilime{Tchooooo)

.[chorus]

Ili Lilime linakhala bwanj\Lokha limamva kukoma limamva kuwawa/
linakhala bwanj\ lokha likhaLiza ndi chimwemwe Liza ndi nkhawa/limandidabwitsa analipanga bwanj/
ndekha ndimazifusa linakhala bwanj/
limadalitsa, limatembelera/
sindilimvetsa ili Lilime/
.
[verse 1]
ca mi tell you say, it's all about dih tongue/
ndimazifusa kwenkwen linakhala bwanj/
limamva kudzuna lokha limamva kuwawa/
lidza ndi chimwemwe lokha libweletsa nkhawa/
limamva kukoma ili limamva sugar/
limakalikira nthawi zinaso kutukwana/
in case yah Neva know Lilime limalenga limapalamula milandu ndi kuzengaso//
.
(B.T.C)
.
(verse 2)
papapa pali la chibwibwi, La litata ili lilaka/
ndimazifunsa linakhala bwanj makamaka/
poti limadalitsa lokha limatembelera/
sindimalimvetsa mumene analilengera/
limagwira ntchito zoposera pa imodz/
limasangalatsa pena kubweletsa misozi/
limafalitsa ma uthenga ambir mbili/
limayamikira pena liipitsa ili/
.
(B.T.C)
.
(Last verse)
Likwiza na mazgo ya chitemwa/
ndeneliro likuswaso mtima/
kachiwalo kokhala mu mlomo/
me tell yah say kanadzadza ndi machimoo/
analipanga bwanj\Lilime/
nanga linakhala bwanj\ Lilime/
nthaw zonse ndimazifusa ineyooo/
.
(B.T.C)
end....
Like my Facebook page
Kommander Zwangie MW

Production Credits: